-
Danieli 4:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 “Uwu ndi uthenga wochokera kwa ine Mfumu Nebukadinezara wopita kwa anthu a mitundu yosiyanasiyana komanso olankhula zinenero zosiyanasiyana amene akukhala padziko lonse lapansi: Mukhale ndi mtendere wochuluka.
-