-
2 Mbiri 36:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Nebukadinezara anatenga ziwiya zina za mʼnyumba ya Yehova nʼkupita nazo ku Babulo ndipo anakaziika mʼnyumba yake yachifumu.+
-
-
Ezara 1:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mfumu Koresi inabweretsanso ziwiya zamʼnyumba ya Yehova. Ziwiyazo nʼzimene Nebukadinezara anatenga ku Yerusalemu nʼkukaziika mʼkachisi wa mulungu wake.+
-