-
Yesaya 47:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Alangizi ako ambirimbiri akutopetsa.
-
-
Danieli 2:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Danieli anayankha mfumuyo kuti: “Palibe amuna anzeru, anthu olankhula ndi mizimu, ansembe ochita zamatsenga kapena anthu okhulupirira nyenyezi amene angakwanitse kukuuzani inu mfumu chinsinsi chimene mukufuna kudziwa.+
-
-
Danieli 5:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Amuna onse anzeru anabwera kwa mfumu koma sanathe kuwerenga mawu amene analembedwawo kapena kuuza mfumu kumasulira kwake.+
-
-
Danieli 5:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ineyo anandibweretsera amuna anzeru ndi anthu okhulupirira mizimu kuti awerenge mawu amene alembedwawa nʼkundiuza kumasulira kwake, koma iwo alephera kumasulira uthenga wake.+
-