-
Amosi 5:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mumasandutsa chilungamo kukhala chitsamba chowawa.
Ndipo mumataya pansi chilungamocho.+
-
-
Amosi 6:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Kodi mahatchi angathamange pathanthwe?
Kapena kodi munthu angalime pathanthwe ndi ngʼombe?
Chifukwa mwasintha chilungamo kukhala chomera chapoizoni,
Ndipo mwasandutsa chipatso cha chilungamo kukhala chinthu chowawa.+
-