-
Yoweli 2:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Ndidzakubwezerani mbewu za zaka zonse
Zimene dzombe, ana a dzombe opanda mapiko komanso dzombe losakaza zinadya.
Limeneli ndi gulu langa lankhondo limene ndinakutumizirani.+
-