Yoweli 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Lengezani nthawi yosala kudya. Itanitsani msonkhano wapadera.+ Sonkhanitsani akulu ndi anthu onse okhala mʼdzikoli,Kuti akumane kunyumba ya Yehova Mulungu wanu+ ndipo alirire Yehova kuti awathandize.
14 Lengezani nthawi yosala kudya. Itanitsani msonkhano wapadera.+ Sonkhanitsani akulu ndi anthu onse okhala mʼdzikoli,Kuti akumane kunyumba ya Yehova Mulungu wanu+ ndipo alirire Yehova kuti awathandize.