-
Mika 1:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Samariya ndidzamusandutsa bwinja,
Malo oyenera kudzalapo mpesa.
Miyala yake ndidzaiponya* mʼchigwa.
Ndipo maziko ake ndidzawafukula nʼkuwasiya pamtunda.
-