-
2 Mafumu 14:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Mʼchaka cha 15 cha Amaziya mwana wa Yehoasi mfumu ya Yuda, Yerobowamu+ mwana wa Yehoasi mfumu ya Isiraeli anakhala mfumu ku Samariya ndipo analamulira zaka 41.
-