Yesaya 30:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo auza anthu oona masomphenya kuti, ‘Lekani kuona masomphenya,’ Ndipo anthu olosera zamʼtsogolo awauza kuti, ‘Musatiuze masomphenya olondola.+ Mutiuze zinthu zotikomera. Muziona masomphenya abodza.+
10 Iwo auza anthu oona masomphenya kuti, ‘Lekani kuona masomphenya,’ Ndipo anthu olosera zamʼtsogolo awauza kuti, ‘Musatiuze masomphenya olondola.+ Mutiuze zinthu zotikomera. Muziona masomphenya abodza.+