-
Yeremiya 1:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ndiyeno Yehova anandiuza kuti:
“Usanene kuti, ‘Ndine mwana,’
Chifukwa ukuyenera kupita kwa anthu onse kumene ndidzakutume,
Ndipo ukanene zonse zimene ndakulamula.+
-