Nahumu 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kuyambira kalekale, Nineve+ anali ngati dziwe la madzi,Koma tsopano anthu ake akuthawa. Ena akufuula kuti: “Taimani! Taimani!” Koma palibe amene akubwerera.+
8 Kuyambira kalekale, Nineve+ anali ngati dziwe la madzi,Koma tsopano anthu ake akuthawa. Ena akufuula kuti: “Taimani! Taimani!” Koma palibe amene akubwerera.+