-
Yobu 38:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ndiye ndinati, ‘Ukhoza kufika apa, koma usapitirirepo,
Ndipo mafunde ako aatali azilekezera pamenepaʼ?+
-
-
Salimo 104:6, 7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Munaliphimba ndi madzi ozama ngati kuti mwaliphimba ndi nsalu.+
Madziwo anakwera kupitirira mapiri.
7 Chifukwa cha kudzudzula kwanu, madziwo anathawa.+
Atamva mabingu anu anayamba kuthawa mopanikizika kwambiri
-
Salimo 107:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Iye amachititsa kuti mphepo yamkuntho ikhale bata,
Mafunde apanyanja amadekha.+
-
-
-