-
Amosi 1:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Iye anati:
“Yehova adzabangula ku Ziyoni,
Ndipo adzafuula ku Yerusalemu.
Malo amene abusa amadyetserako ziweto adzalira,
Ndipo pansonga ya phiri la Karimeli padzauma.”+
-