Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Deuteronomo 30:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Yehova Mulungu wanu adzachititsa kuti zinthu zikuyendereni bwino kwambiri pa ntchito iliyonse ya manja anu.+ Adzachulukitsa ana anu, ziweto zanu ndi zokolola zanu, chifukwa Yehova adzasangalalanso kuchititsa kuti zinthu zikuyendereni bwino, ngati mmene anachitira ndi makolo anu.+

  • Salimo 147:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yehova amasangalala ndi anthu amene amamuopa,+

      Amene amayembekezera chikondi chake chokhulupirika.+

  • Yesaya 62:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Udzakhala chisoti chokongola mʼdzanja la Yehova,

      Ndiponso nduwira yachifumu mʼdzanja la Mulungu wako.

  • Yesaya 65:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Yeremiya 32:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Ndidzasangalala nawo ndipo ndidzawachitira zabwino.+ Ndidzawachititsa kuti azikhala mʼdziko lino+ mpaka kalekale. Ndidzachita zimenezi ndi mtima wanga wonse komanso moyo wanga wonse.’”

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani