Salimo 47:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chifukwa Yehova, Wamʼmwambamwamba ndi wochititsa mantha,+Iye ndi Mfumu yaikulu padziko lonse lapansi.+ Yeremiya 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Yehova ndi Mulungu woonadi. Iye ndi Mulungu wamoyo+ ndipo ndi Mfumu yamuyaya.+ Dziko lapansi lidzagwedezeka chifukwa cha mkwiyo wake,+Ndipo palibe mitundu ya anthu imene idzapilire mkwiyo wake.
2 Chifukwa Yehova, Wamʼmwambamwamba ndi wochititsa mantha,+Iye ndi Mfumu yaikulu padziko lonse lapansi.+
10 Koma Yehova ndi Mulungu woonadi. Iye ndi Mulungu wamoyo+ ndipo ndi Mfumu yamuyaya.+ Dziko lapansi lidzagwedezeka chifukwa cha mkwiyo wake,+Ndipo palibe mitundu ya anthu imene idzapilire mkwiyo wake.