Yeremiya 49:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano amuna inu, tamverani zimene Yehova wasankha* kuchitira Edomu ndiponso zimene waganiza kuti achitire anthu amene akukhala ku Temani:+ Ndithudi, chilombo chidzakokera kutali ana a nkhosa. Adzachititsa kuti malo awo okhala asanduke bwinja chifukwa cha zimene anthuwo anachita.+ Yoweli 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Iguputo adzasanduka bwinja,+Ndipo Edomu adzakhala chipululu chopanda kanthu.+Chifukwa cha nkhanza zimene anachitira anthu a ku Yuda,+Ndiponso chifukwa chokhetsa magazi a anthu osalakwa mʼdziko la Yudalo.+
20 Tsopano amuna inu, tamverani zimene Yehova wasankha* kuchitira Edomu ndiponso zimene waganiza kuti achitire anthu amene akukhala ku Temani:+ Ndithudi, chilombo chidzakokera kutali ana a nkhosa. Adzachititsa kuti malo awo okhala asanduke bwinja chifukwa cha zimene anthuwo anachita.+
19 Koma Iguputo adzasanduka bwinja,+Ndipo Edomu adzakhala chipululu chopanda kanthu.+Chifukwa cha nkhanza zimene anachitira anthu a ku Yuda,+Ndiponso chifukwa chokhetsa magazi a anthu osalakwa mʼdziko la Yudalo.+