-
Yesaya 34:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Usiku kapena masana motowo sudzazimitsidwa.
Utsi wake udzapitiriza kukwera mʼmwamba mpaka kalekale.
Dzikolo lidzakhala lowonongedwa ku mibadwomibadwo.
Mpaka muyaya, palibe amene adzadutsemo.+
-
-
Yesaya 34:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Minga zidzamera pansanja zake zokhala ndi mpanda wolimba,
Zomera zoyabwa ndi zitsamba zaminga zidzamera pamalo ake otetezeka.
Iye adzakhala malo okhala mimbulu,+
Ndi malo obisalamo nthiwatiwa.
-