Ekisodo 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Levitiko 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munthu akatemberera* bambo kapena mayi ake, aziphedwa ndithu.+ Mlandu wa magazi ake ukhale pa iye chifukwa watemberera bambo ake kapena mayi ake.
9 Munthu akatemberera* bambo kapena mayi ake, aziphedwa ndithu.+ Mlandu wa magazi ake ukhale pa iye chifukwa watemberera bambo ake kapena mayi ake.