-
Yeremiya 31:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 “Taonani! Masiku akubwera, pamene ndidzachita pangano latsopano ndi nyumba ya Isiraeli komanso nyumba ya Yuda,” akutero Yehova.+
-