Yesaya 40:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Winawake akufuula mʼchipululu kuti: “Konzani njira ya Yehova!+ Mulungu wathu mukonzereni msewu wowongoka+ wodutsa mʼchipululu.+ Yohane 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
3 Winawake akufuula mʼchipululu kuti: “Konzani njira ya Yehova!+ Mulungu wathu mukonzereni msewu wowongoka+ wodutsa mʼchipululu.+