-
Deuteronomo 18:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Yehova Mulungu wanu adzakupatsani mneneri ngati ine kuchokera pakati pa abale anu, ndipo mudzamumvere mneneri ameneyo.+
-