Yesaya 42:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndikumuthandiza, Wosankhidwa wanga+ amene amandisangalatsa,+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye.+Iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+ Mateyu 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yohane 1:32-34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndikumuthandiza, Wosankhidwa wanga+ amene amandisangalatsa,+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye.+Iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+