Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 2 Samueli 5:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Davide atachoka ku Heburoni nʼkupita ku Yerusalemu anakwatiranso akazi ena komanso anali ndi akazi apambali+ ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi.+ 14 Ana amene Davide anabereka ku Yerusalemu ndi awa: Samuwa, Sobabu, Natani,+ Solomo,+

  • 1 Mbiri 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ku Yerusalemu+ iye anabereka ana awa: Simeya, Sobabu, Natani+ ndi Solomo.+ Ana 4 amenewa mayi awo anali Bati-seba+ mwana wa Amiyeli.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani