Danieli 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako ndinamva mawu a munthu kuchokera pakati pa mtsinje wa Ulai.+ Iye anaitana kuti: “Gabirieli,+ munthuyo umuthandize kuti amvetsetse zimene waona.”+ Luka 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
16 Kenako ndinamva mawu a munthu kuchokera pakati pa mtsinje wa Ulai.+ Iye anaitana kuti: “Gabirieli,+ munthuyo umuthandize kuti amvetsetse zimene waona.”+