-
Yesaya 8:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Iye adzakhala ngati malo opatulika,
Koma kwa nyumba zonse ziwiri za Isiraeli,
Adzakhala ngati mwala wopunthwitsa+
Ndiponso ngati thanthwe lokhumudwitsa.
Adzakhala ngati msampha komanso khwekhwe
Kwa anthu okhala mu Yerusalemu.
-