-
Levitiko 24:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Choncho munthu amene wanyoza dzina la Yehova aziphedwa ndithu.+ Gulu lonse lizimuponya miyala. Kaya ndi mlendo wokhala pakati panu kapena nzika, aziphedwa chifukwa chonyoza Dzinalo.
-