Salimo 69:22, 23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tebulo lawo likhale msampha kwa iwo,Ndipo zinthu zimene zikuwayendera bwino zikhale ngati khwekhwe kwa iwo.+ 23 Maso awo achite mdima kuti asaone,Ndipo chititsani miyendo yawo kuti izinjenjemera* nthawi zonse.
22 Tebulo lawo likhale msampha kwa iwo,Ndipo zinthu zimene zikuwayendera bwino zikhale ngati khwekhwe kwa iwo.+ 23 Maso awo achite mdima kuti asaone,Ndipo chititsani miyendo yawo kuti izinjenjemera* nthawi zonse.