-
Deuteronomo 32:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Iwo ankapereka nsembe kwa ziwanda, osati kwa Mulungu.+
Anapereka nsembe kwa milungu imene sankaidziwa,
Kwa milungu yatsopano yongobwera kumene,
Komanso kwa milungu imene makolo anu sankaidziwa.
-