Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Danieli 3:23-25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Koma amuna atatuwa, Shadireki, Misheki ndi Abedinego, anagwera mungʼanjo ya motoyo ali omangidwa.

      24 Ndiyeno Mfumu Nebukadinezara inachita mantha kwambiri ndipo inanyamuka mwachangu nʼkufunsa nduna zake zapamwamba kuti: “Kodi sitinaponye amuna atatu pamoto titawamanga?” Ndunazo zinayankha mfumuyo kuti: “Inde, mfumu.” 25 Ndiyeno mfumu inati: “Taonani! Inetu ndikuona amuna 4 akuyendayenda pakati pa moto ali osamangidwa komanso sakupsa, ndipo munthu wa 4 akuoneka ngati mwana wa milungu.”

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani