Yesaya 40:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye adzasamalira* gulu la nkhosa zake ngati mʼbusa.+ Ndi dzanja lake, adzasonkhanitsa pamodzi ana a nkhosa,Ndipo adzawanyamulira pachifuwa pake. Nkhosa zimene zikuyamwitsa adzazitsogolera mwachikondi.+ Yohane 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Machitidwe 20:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
11 Iye adzasamalira* gulu la nkhosa zake ngati mʼbusa.+ Ndi dzanja lake, adzasonkhanitsa pamodzi ana a nkhosa,Ndipo adzawanyamulira pachifuwa pake. Nkhosa zimene zikuyamwitsa adzazitsogolera mwachikondi.+