Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yobu 39:9-11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Kodi ngʼombe yamphongo yamʼtchire imafunitsitsa kukutumikira?+

      Kodi ingagone usiku wonse mʼkhola lako?*

      10 Kodi ungamange ngʼombe yamʼtchire ndi zingwe kuti ikulimire mizere,

      Kapena kodi ingalole kuti upite nayo kuchigwa kukalima?

      11 Kodi ungaikhulupirire chifukwa ili ndi mphamvu zochuluka,

      Nʼkuisiya kuti ikugwirire ntchito yako yotopetsa?

  • Chivumbulutso 6:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani