-
Yobu 39:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Kapena kodi chiwombankhanga chimauluka mʼmwamba chifukwa choti iweyo wachilamula,+
Nʼkukamanga chisa chake pamwamba kwambiri?+
-
Yobu 39:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Chili pamalo omwewo, chimafunafuna chakudya,+
Maso ake amaona kutali kwambiri.
-
-
-