Yesaya 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Taonani zimene zikubwera: Kukubwera amuna amene akwera galeta lankhondo limene likukokedwa ndi mahatchi awiri.”+ Kenako iye analankhula kuti: “Wagwa! Babulo wagwa!+ Zifaniziro zonse zogoba za milungu yake zaphwanyidwa ndipo zili pansi.”+ Chivumbulutso 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
9 Taonani zimene zikubwera: Kukubwera amuna amene akwera galeta lankhondo limene likukokedwa ndi mahatchi awiri.”+ Kenako iye analankhula kuti: “Wagwa! Babulo wagwa!+ Zifaniziro zonse zogoba za milungu yake zaphwanyidwa ndipo zili pansi.”+