Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Akorinto 13
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la 1 Akorinto

      • Chikondi—njira yopambana (1-13)

1 Akorinto 13:1

Mawu a M'munsi

  • *

    Mʼchilankhulo choyambirira, “malilime.”

1 Akorinto 13:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 12:8
  • +1Yo 4:20

1 Akorinto 13:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 6:2
  • +2Ak 9:7

1 Akorinto 13:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Yo 4:8
  • +1At 5:14
  • +Aro 13:10; Aef 4:32
  • +Aga 5:26
  • +1Pe 5:5

1 Akorinto 13:5

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “mwano.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 13:13; 1Ak 14:40
  • +1Ak 10:24; Afi 2:4
  • +Mt 5:39; Yak 1:19
  • +Aef 4:32; Akl 3:13

1 Akorinto 13:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 12:9

1 Akorinto 13:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Pe 4:8
  • +Mac 17:11
  • +Aro 8:25; 12:12
  • +1At 1:3

1 Akorinto 13:8

Mawu a M'munsi

  • *

    Kutanthauza kulankhula zilankhulo zosiyanasiyana modabwitsa.

1 Akorinto 13:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Miy 4:18

1 Akorinto 13:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 22:37; Aro 13:10

Malemba Ena

1 Akor. 13:21Ak 12:8
1 Akor. 13:21Yo 4:20
1 Akor. 13:3Mt 6:2
1 Akor. 13:32Ak 9:7
1 Akor. 13:41Yo 4:8
1 Akor. 13:41At 5:14
1 Akor. 13:4Aro 13:10; Aef 4:32
1 Akor. 13:4Aga 5:26
1 Akor. 13:41Pe 5:5
1 Akor. 13:5Aro 13:13; 1Ak 14:40
1 Akor. 13:51Ak 10:24; Afi 2:4
1 Akor. 13:5Mt 5:39; Yak 1:19
1 Akor. 13:5Aef 4:32; Akl 3:13
1 Akor. 13:6Aro 12:9
1 Akor. 13:71Pe 4:8
1 Akor. 13:7Mac 17:11
1 Akor. 13:7Aro 8:25; 12:12
1 Akor. 13:71At 1:3
1 Akor. 13:9Miy 4:18
1 Akor. 13:13Mt 22:37; Aro 13:10
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
1 Akorinto 13:1-13

Kalata Yoyamba Yopita kwa Akorinto

13 Ngati ndimalankhula zilankhulo* za anthu ndi angelo koma ndilibe chikondi, ndili ngati belu longolira kapena chinganga chosokosera. 2 Ndipo ngati ndili ndi mphatso yonenera, yomvetsa zinsinsi zonse zopatulika komanso yodziwa zinthu zonse,+ ndipo ndili ndi chikhulupiriro cholimba moti ndingathe kusuntha mapiri, koma ndilibe chikondi, zomwe ndimachita zilibe ntchito.+ 3 Ngati ndingapereke zinthu zanga zonse kuti ndidyetse ena,+ ndipo ngati ndingapereke thupi langa kuti ndidzitame, koma ndilibe chikondi,+ sindingapindule chilichonse.

4 Chikondi+ nʼcholeza mtima+ ndiponso nʼchokoma mtima.+ Chikondi sichichita nsanje,+ sichidzitama, sichidzikuza,+ 5 sichichita zosayenera,*+ sichisamala zofuna zake zokha,+ sichikwiya+ ndipo sichisunga zifukwa.+ 6 Sichisangalala ndi zosalungama,+ koma chimasangalala ndi choonadi. 7 Chimakwirira zinthu zonse,+ chimakhulupirira zinthu zonse,+ chimayembekezera zinthu zonse+ komanso chimapirira zinthu zonse.+

8 Chikondi sichitha. Koma kaya pali mphatso za kunenera, zidzatha. Kaya Kulankhula malilime,* kudzatha. Ngakhale mphatso yodziwa zinthu, idzatha. 9 Chifukwa sitikudziwa zonse+ ndipo tikunenera moperewera. 10 Koma tikadzadziwa zonse, zoperewerazi zidzatha. 11 Pamene ndinali mwana, ndinkalankhula ngati mwana, kuganiza ngati mwana ndiponso kuona zinthu ngati mwana. Koma mmene ndakulamu, ndasiya zachibwana. 12 Panopa sitikuona bwinobwino chifukwa tikugwiritsa ntchito galasi losaoneka bwino, koma pa nthawiyo tizidzaona bwinobwino. Panopa sindikudziwa zonse, koma pa nthawiyo ndidzadziwa zonse ngati mmene Mulungu akundidziwira ineyo. 13 Komabe, tsopano patsala zitatu izi: Chikhulupiriro, chiyembekezo ndi chikondi. Koma chachikulu pa zonsezi ndi chikondi.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani