YOHANE
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
-
Yudasi anapereka Yesu (1-9)
Petulo anagwiritsa ntchito lupanga (10, 11)
Yesu anamupititsa kwa Anasi (12-14)
Petulo anakana Yesu koyamba (15-18)
Yesu anaonekera pamaso pa Anasi (19-24)
Petulo anakana Yesu kachiwiri ndi kachitatu (25-27)
Yesu anaonekera pamaso pa Pilato (28-40)
“Ufumu wanga si wamʼdzikoli” (36)