Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Zimene Zili Mʼbuku la 2 Petulo 2 PETULO ZIMENE ZILI MʼBUKULI 1 Moni (1) Mupitirizebe kukhala pakati pa anthu oitanidwa (2-15) Makhalidwe ofunika kuwonjezera pa chikhulupiriro (5-9) Mawu aulosi adzakwaniritsidwa (16-21) 2 Kudzakhala aphunzitsi abodza (1-3) Umboni wotsimikizira kuti aphunzitsi abodza adzaweruzidwa (4-10a) Angelo anawaponya mu Tatalasi (4) Chigumula; Sodomu ndi Gomora (5-7) Mmene tingadziwire aphunzitsi abodza (10b-22) 3 Anthu onyoza amakayikira zoti anthu oipa adzawonongedwa (1-7) Yehova sakuchedwa (8-10) Ganizirani za mtundu wa anthu amene muyenera kukhala (11-16) Kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano (13) Chenjerani kuti anthu asakusocheretseni (17, 18)