FUNSO 20
Mungatani kuti muzipindula mukamawerenga Baibulo?
MUKAMAWERENGA BAIBULO MUZIDZIFUNSA MAFUNSO AWA:
Kodi ndikuphunzirapo chiyani zokhudza Yehova Mulungu?
Kodi malembawa akugwirizana bwanji ndi uthenga wa mʼBaibulo lonse?
Kodi zimene ndawerengazi ndingazigwiritse ntchito bwanji?
Kodi ndingagwiritse ntchito bwanji malembawa pothandiza anthu ena?
“Mawu anu ndi nyale younikira kumapazi anga, komanso kuwala kounikira njira yanga.”