February 5-11
MATEYU 12-13
- Nyimbo Na. 27 ndi Pemphero 
- Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.) 
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
- “Fanizo la Tirigu ndi Namsongole”: (10 min.) - Mat. 13:24-26—Munthu anafesa mbewu zabwino m’munda mwake, koma mdani wake anabwera n’kudzafesamo namsongole (w13 7/15 9-10 ¶2-3) 
- Mat. 13:27-29—Tirigu ndi namsongole zinakulira pamodzi mpaka nthawi yokolola (w13 7/15 10 ¶4) 
- Mat. 13:30—Nthawi yokolola itafika, okolola anasonkhanitsa namsongole kenako anasonkhanitsa tirigu (w13 7/15 12 ¶10-12) 
 
- Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.) - Mat. 12:20—Kodi tingatsanzire bwanji khalidwe la Yesu lochitira ena chifundo? (“nyale yofuka” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 12:20, nwtsty) 
- Mat. 13:25—Kodi zinkachitikadi kuti munthu ankafesa namsongole m’munda umene mnzake wafesamo tirigu? (w16.10 32) 
- Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno? 
- Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno? 
 
- Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mat. 12:1-21 
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
- Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi. 
- Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene. 
- Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 22-23 ¶10-12 
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
- Zofunika Pampingo: (5 min.) 
- “Mfundo Zimene Tingaphunzire Kuchokera M’mafanizo Onena za Ufumu”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Kambiranani mmene mafanizo amenewa angatithandizire kuti tizichita khama polalikira. 
- Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 13 ¶33-34 ndi bokosi patsamba “145 komanso tsamba 146-147 
- Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.) 
- Nyimbo Na. 10 ndi Pemphero