May 7-13
MALIKO 7-8
Nyimbo Na. 13 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Nyamula Mtengo Wako Wozunzikirapo, ndi Kunditsatira Mosalekeza”: (10 min.)
Maliko 8:34—Kuti tikhale wotsatira wa Yesu tiyenera kudzikana tokha (“adzikane yekha” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 8:34, nwtsty; w92 8/1 17 ¶14)
Maliko 8:35-37—Yesu anafunsa mafunso awiri ofunika amene angatithandize kuti tiziika zinthu zofunika kwambiri pa malo oyamba (w08 10/15 25-26 ¶3-4)
Maliko 8:38—Pamafunika kulimba mtima kuti tikhale otsatira a Khristu (jy 143 ¶4)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Maliko 7:5-8—N’chifukwa chiyani kusamba m’manja inali nkhani yaikulu kwa Afarisi? (w16.08 30 ¶1-4)
Maliko 7:32-35—Kodi tikuphunzirapo chiyani pa zimene Yesu anachita posonyeza kuganizira munthu wina wogontha? (w00 2/15 17-18 ¶9-11)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Maliko 7:1-15
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 165-166 ¶6-7
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (5 min.)
“Muzithandiza Ana Anu Kuti Akhale Otsatira a Khristu”: (10 min.) Nkhani yokambirana.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 17 ¶19-20 komanso tsamba 187, 188-191
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 60 ndi Pemphero