Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb18.05 4
  • May 14-20

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 14-20
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18.05 4

May 14-20

Maliko 9-10

  • Nyimbo Na. 22 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Masomphenya Olimbitsa Chikhulupiriro”: (10 min.)

    • Maliko 9:1​—Yesu analonjeza atumwi ake ena kuti adzaona ulemerero umene adzakhale nawo mu Ufumu wake (w05 1/15 12 ¶9-10)

    • Maliko 9:2-6​—Pamene Yesu anasandulika, Petulo, Yakobo ndi Yohane anaona Yesu akuyankhulana ndi “Eliya” komanso “Mose” (w05 1/15 12 ¶11)

    • Maliko 9:7​—Yehova anatsimikizira anthuwa ndi mawu ake kuti Yesu ndi Mwana wake (“Mawu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 9:7, nwtsty)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Maliko 10:6-9​—Kodi ndi mfundo iti yokhudza ukwati yomwe Yesu anaitchula palembali? (w08 2/15 30 ¶8)

    • Maliko 10:17, 18​—N’chifukwa chiyani Yesu anakana, munthu wina atamutchula kuti “Mphunzitsi Wabwino”? (“Mphunzitsi Wabwino” “Palibe wabwino koma Mulungu yekha” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 10:17, 18, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Maliko 9:1-13

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w04 5/15 30-31​—Mutu: Kodi Mawu a Yesu Opezeka pa Maliko 10:25 Amatanthauza Chiyani?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 131

  • “Chimene Mulungu Wachimanga Pamodzi . . . ”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Chikondi ndi Ulemu Zimachititsa Banja Kukhala Logwirizana.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 18 ¶1-8 komanso tsamba 192-193

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 66 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani