Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb18.11 2
  • November 5-11

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • November 5-11
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18.11 2

November 5-11

YOHANE 20-21

  • Nyimbo Na. 35 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Umandikonda Ine Kuposa Izi?”: (10 min.)

    • Yoh. 21:1-3​—Yesu atangophedwa, Petulo ndi ophunzira ena anapita kukapha nsomba

    • Yoh. 21:4-14​—Yesu ataukitsidwa, anaonekera kwa Petulo komanso ophunzira ena

    • Yoh. 21:15-19​—Yesu anathandiza Petulo kudziwa zinthu zimene ankayenera kuziika patsogolo m’moyo wake (“Yesu anafunsa Simoni Petulo kuti” “kodi umandikonda ine kuposa izi?” “kachitatu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 21:15, 17, nwtsty)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yoh. 20:17​—Kodi mawu omwe Yesu anauza Mariya Mmagadala akutanthauza chiyani? (“Usandikangamire” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh 20:17, nwtsty)

    • Yoh. 20:28​—N’chifukwa chiyani Tomasi anatchula Yesu kuti “Mbuyanga ndi Mulungu wanga!” (“Mbuyanga ndi Mulungu wanga!” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 20:28, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yoh. 20:1-18

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 79 ¶21-22. Kenako muitanireni kumisonkhano yathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 37

  • Zofunika Pampingo: (15 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 12

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 52 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani