Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb19.04 2
  • Kusakhala Pabanja ndi Mphatso

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kusakhala Pabanja ndi Mphatso
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani Yokhala Pabanja Ndi Kusakhala Pabanja?
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
  • Muziona Kuti Anthu Ena Ndi Ofunika Mumpingo
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2020
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19.04 2

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 1 AKORINTO 7-9

Kusakhala Pabanja ndi Mphatso

7:32, 35, 38

Kwa nthawi yaitali, Akhristu ambiri akhala akunena kuti kusakhala pabanja kumawapatsa mpata wochita zambiri potumikira Yehova. Amanenanso kuti kumawathandiza kuti adziwane ndi anthu ambiri komanso kuti azikonda kwambiri Yehova.

Abale atatu osakwatira ali paulendo wokalalikira ku Australia mu 1937; mlongo wosakwatiwa akufika ku Mexico mu 1947 kukachita utumiki waumishonale

mu 1937, abale ali paulendo wokalalikira ku Australia; mu 1947, mlongo amene anamaliza maphunziro a sukulu ya Giliyadi akufika ku Mexico

M’bale wosakwatira akulalikira ku Brazil; ophunzira omwe sali pabanja ali ku Sukulu ya Akhristu Olalikira za Ufumu ku Malawi

m’bale akulalikira ku Brazil; ali ku Sukulu ya Akhristu Olalikira za Ufumu ku Malawi

MAFUNSO OFUNIKA KUWAGANIZIRA: Ngati simuli pabanja, kodi mungatani kuti muzigwiritsa ntchito nthawi imeneyi mwanzeru?

Kodi abale ndi alongo mumpingo angathandize bwanji anthu amene sali pabanja?

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani