Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb19.04 3
  • Yehova ndi Wokhulupirika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yehova ndi Wokhulupirika
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Kukhala Okhulupirika kwa Yehova Kumabweretsa Madalitso
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Kodi Mzimu Woyera Umatithandiza Bwanji?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19.04 3

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 1 AKORINTO 10-13

Yehova ndi Wokhulupirika

10:13

Mlongo akuganizira za mayesero omwe wakumana nawo ndipo akupemphera kuti Mulungu amuthandize, kenako akupita mu utumiki ndi mlongo wina

Ngakhale kuti Yehova akhoza kutichotsera mayesero, nthawi zambiri amapereka “njira yopulumukira.” Iye amachita zimenezi potipatsa zinthu zofunikira kuti tithe kupirira mayesero omwe takumana nawo.

  • Angatithandize kuti maganizo ndi mtima wathu zikhale m’malo pogwiritsa ntchito Mawu ake, mzimu wake woyera komanso zinthu zauzimu zomwe amatipatsa.​—Mat. 24:45; Yoh. 14:16; Aroma 15:4

  • Akhoza kutitsogolera pogwiritsa ntchito mzimu woyera womwe ungatithandize kukumbukira mfundo komanso zitsanzo za anthu a m’Baibulo. Angatithandizenso kuganizira njira yabwino yomwe tingasankhe.​—Yoh. 14:26

  • Akhozanso kugwiritsa ntchito angelo ake kuti atithandize.​—Aheb. 1:14

  • Angagwiritsenso ntchito abale ndi alongo athu.​—Akol. 4:11

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani