Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb19.05 2
  • May 6-12

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 6-12
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19.05 2

May 6-12

2 Akorinto 4-6

  • Nyimbo Na. 128 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Sitikubwerera M’mbuyo”: (10 min.)

    • 2 Akor. 4:16​—“Tsiku ndi tsiku” Yehova amatithandiza kukhalanso atsopano (w04 8/15 25 ¶16-17)

    • 2 Akor. 4:17​—Mavuto omwe tikukumana nawowa ndi ‘akanthawi komanso opepuka’ (it-1 724-725)

    • 2 Akor. 4:18​—Tiziganizira madalitso a Ufumu omwe tidzapeze mtsogolo

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • 2 Akor. 4:7​—Kodi chuma chomwe chili “m’zonyamulira zoumbidwa ndi dothi” n’chiyani? (w12 2/1 28-29)

    • 2 Akor. 6:13​—Kodi tingatsatire bwanji malangizo akuti “futukulani mtima wanu”? (w09 11/15 21 ¶7)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) 2 Akor. 4:1-15 (th phunziro 12)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kuwerenga Molondola, kenako kambiranani phunziro 5 m’kabuku ka Kuphunzitsa.

  • Nkhani: (Osapitirira 5 min.) w04 7/1 30-31​—Mutu: Kodi Mkhristu Wobatizidwa Angakhale pa Chibwenzi ndi Wofalitsa Wosabatizidwa? (th phunziro 7)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 143

  • Ndimachita Zonse Zomwe Ndingathe: (8 min.) Onerani vidiyoyi. Kenako kambiranani mafunso otsatirawa: Kodi m’bale Foster anasonyeza bwanji kuti anadzipereka kwambiri potumikira Yehova ali wachinyamata? Kodi zinthu zinasintha bwanji pa moyo wake? Kodi panopa akuchita zotani potumikira Yehova ngakhale kuti zinthu zinasintha pa moyo wake? Kodi mwaphunzira zotani pa zomwe zinachitikira m’bale Foster?

  • Zofunika Pampingo: (7 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs 4:12-17 ndi mfundo zakumapeto

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 93 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani