April 19-25
NUMERI 22-24
- Nyimbo Na. 8 ndi Pemphero 
- Mawu Oyamba (1 min.) 
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
- “Yehova Amasintha Temberero N’kukhala Dalitso”: (10 min.) 
- Mfundo Zothandiza: (10 min.) - Nu 22:20-22—N’chifukwa chiyani Yehova anakwiyira kwambiri Balamu? (w04 8/1 27 ¶2) 
- Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina? 
 
- Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Nu 23:11-18 (th phunziro 2) 
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
- “Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki—Muzigwiritsa Ntchito Mawu a Mulungu”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Muziwonjezera Luso Lanu Kuti Muzisangalala ndi Ntchito Yophunzitsa—Muzigwiritsa Ntchito Mawu a Mulungu. 
- Phunziro la Baibulo: (5 min.) fg phunziro 5:3-4 (th phunziro 6) 
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
- “Yehova Amasintha Chizunzo N’kukhala Mwayi Wolalikira”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kucheza ndi Dmitriy Mikhaylov. 
- Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia 19:12-20 
- Mawu Omaliza (3 min.) 
- Nyimbo Na. 79 ndi Pemphero