Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb22.01 9
  • January 24-30

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • January 24-30
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22.01 9

January 24-30

RUTE 1-2

  • Nyimbo Na. 108 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzisonyeza Chikondi Chokhulupirika”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Ru 1:20, 21​—N’chifukwa chiyani Naomi ananena kuti Yehova wachititsa moyo wake kukhala owawa? (w05 3/1 27 ¶1)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Ru 1:1-17 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 12)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? (th phunziro 9)

  • Nkhani: (5 min.) ia 5:5-9​—Mutu: Kodi Tikati Banja N’chiyani? (th phunziro 20)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 54

  • “Yehova Amatisonyeza Chikondi Chokhulupirika”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Lipoti la Komiti ya Ogwirizanitsa la 2019.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 10:9-18, Zakumapeto 25

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 137 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani