Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb22.05 24
  • June 27–July 3

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • June 27–July 3
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22.05 24

June 27–July 3

2 SAMUELI 15-17

  • Nyimbo Na. 123 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Abisalomu Anaukira Chifukwa cha Kunyada”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Sa 16:4​—Kodi tikuphunzirapo chiyani pa mmene Davide anachitira zinthu mopupuluma? (w18.08 1:11)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Sa 17:17-23 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 7)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? (th phunziro 2)

  • Nkhani: (5 min.) w09 5/15 27-28​—Mutu: Muzichita Zinthu Mwakhama Ngati Itai Mukakhala mu Utumiki.​—2Sa 15:19-22. (th phunziro 13)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 106

  • Zofunika Pampingo: (5 min.)

  • “Chikondi . . . Sichidzikuza”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzikumbukira Zimene Chikondi Chimachita Komanso Zimene Sichichita​—Sichidzikuza.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs 17:9-15

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 38 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani