Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb23.01 23
  • February 27–March 5

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • February 27–March 5
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23.01 23

February 27–March 5

1 MBIRI 20-22

  • Nyimbo Na. 133 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzithandiza Achinyamata Kuti Azichita Zambiri”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 1Mb 21:15​—Kodi lembali likutiphunzitsa chiyani zokhudza Yehova? (w05-CN 10/1 11:6)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mb 20:1-8 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 1)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. M’patseni kapepala komuitanira kumisonkhano yathu ndipo yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti, Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani? kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 19)

  • Nkhani: (5 min.) w16.03 10-11:10-15​—Mutu: Achinyamata, Yesetsani Kuti Mubatizidwe. (th phunziro 16)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 134

  • “Muzigwiritsa Ntchito Mfundo za M’Baibulo Pothandiza Ana Anu Kuti Zinthu Ziwayendere Bwino”: (10 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.

  • Zofunika Pampingo: (5 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 31

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 74 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani