Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb23.07 2
  • July 3-9

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • July 3-9
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23.07 2

July 3-9

EZARA 4-6

  • Nyimbo Na. 148 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Musakalowerere Ntchito Yomanga”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Eza 6:13​—N’chifukwa chiyani mawu akuti “kutsidya lina la Mtsinje” ali ochititsa chidwi? (w93-CN 6/15 32:3-5)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Eza 4:8-15 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya Ulendo Woyamba: Kuvutika​—Yak 1:13. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mufotokozereni za webusaiti yathu ya jw.org, ndipo mugawireni khadi lodziwitsa anthu za webusaitiyi. (th phunziro 1)

  • Ulendo Woyamba: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Muuzeni kuti timaphunzira Baibulo ndi anthu ndipo m’patseni khadi lodziwitsa anthu za phunziro la Baibulo. (th phunziro 9)

MOYO WATHU WACHIKHRIS

  • Nyimbo Na. 7

  • “Kuteteza . . . ndi Kukhazikitsa Mwalamulo Ntchito ya Uthenga Wabwino”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 44:1-4 ndi Mawu akumapeto

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 39 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani