NUMERI
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
-  1  - 
- Kalembera wa amuna oyenera kupita kunkhondo (1-46) 
- Alevi sankayenera kupita nawo kunkhondo (47-51) 
- Dongosolo lomangira matenti mumsasa (52-54) 
 
-  2  
-  3  
-  4  - 
- Utumiki wa Akohati (1-20) 
- Utumiki wa Agerisoni (21-28) 
- Utumiki wa Amerari (29-33) 
- Mmene kalembera anayendera (34-49) 
 
-  5  - 
- Kuika munthu wodetsedwa kwayekha (1-4) 
- Kuulula tchimo komanso kulipira (5-10) 
- Kumwetsa madzi munthu amene akumuganizira kuti wachita chigololo (11-31) 
 
-  6  
-  7  
-  8  - 
- Aroni anayatsa nyale 7 (1-4) 
- Alevi anayeretsedwa nʼkuyamba kutumikira (5-22) 
- Zaka zimene Alevi ankayenera kuyamba komanso kusiya utumiki (23-26) 
 
-  9  
- 10  - 
- Malipenga asiliva (1-10) 
- Anachoka ku Sinai (11-13) 
- Dongosolo la kayendedwe (14-28) 
- Hobabu anapemphedwa kuti alondolere njira Aisiraeli (29-34) 
- Pemphero limene Mose anapereka ponyamuka (35, 36) 
 
- 11  - 
- Mulungu anawabweretsera moto chifukwa chodandaula (1-3) 
- Anthu anayamba kulirira nyama (4-9) 
- Mose ankadziona kuti ndi wosayenerera (10-15) 
- Yehova anapereka mzimu kwa akulu 70 (16-25) 
- Eledadi ndi Medadi; Yoswa anachita nsanje chifukwa choti ankadera nkhawa Mose (26-30) 
- Anabweretsa zinziri; anthu analangidwa chifukwa cha dyera (31-35) 
 
- 12  - 
- Miriamu ndi Aroni anakangana ndi Mose (1-3) 
- Yehova anaikira kumbuyo Mose (4-8) 
- Miriamu anachita khate (9-16) 
 
- 13  
- 14  - 
- Anthu ankafuna kubwerera ku Iguputo (1-10) 
- Yehova anakwiya; Mose anapepesa (11-19) 
- Chilango: zaka 40 mʼchipululu (20-38) 
- Aisiraeli anagonjetsedwa ndi Aamaleki (39-45) 
 
- 15  - 
- Malamulo okhudza nsembe (1-21) 
- Nsembe za machimo amene munthu wachita mosadziwa (22-29) 
- Chilango cha munthu amene wachimwa mwadala (30, 31) 
- Munthu amene anaphwanya Sabata anamupha (32-36) 
- Zovala zizikhala ndi ulusi mʼmphepete (37-41) 
 
- 16  
- 17  
- 18  - 
- Ntchito za ansembe ndi Alevi (1-7) 
- Gawo limene ansembe ankalandira (8-19) 
- Alevi azilandira komanso kupereka chakhumi (20-32) 
 
- 19  
- 20  - 
- Miriamu anamwalira ku Kadesi (1) 
- Mose anamenya thanthwe nʼkuchimwa (2-13) 
- Aedomu anakana kuti Aisiraeli adutse mʼdziko lawo (14-21) 
- Imfa ya Aroni (22-29) 
 
- 21  - 
- Mfumu ya ku Aradi inagonjetsedwa (1-3) 
- Njoka yakopa (4-9) 
- Aisiraeli anayenda mozungulira Mowabu (10-20) 
- Sihoni Mfumu ya Aamori inagonjetsedwa (21-30) 
- Ogi Mfumu ya Aamori inagonjetsedwa (31-35) 
 
- 22  
- 23  
- 24  
- 25  
- 26  
- 27  
- 28  
- 29  
- 30  
- 31  
- 32  
- 33  
- 34  
- 35  
- 36